Dokotala wa anthu odwala matenda a m’bongo/mzimu (en. Psychiatrist)

Dokotala/sing’anga wa anthu odwala matenda a m’bongo/mzimu (en. Psychiatrist)

Dokotala kapena ng’anga amene anaphunzira maphunziro apadera oyeza, kupewetsa ndi kuchiza anthu odwala matenda a m’bongo kapena mzimu amatchedwa psychiatrist muchiyankhulo cha English.

165 copy

 

Author: chipikadzongwe

Psychiatrist